DedzaFrom Wikipedia, the free encyclopedia Dedza ndi boma lina la dziko la Malawi. Dedza Golomoti escarpment ku Dedza. Bomali liri pa malire ndi maboma a Ntcheu, Lilongwe, Salima, Mangochi, Balaka Komanso Mozambique. Anthu ambiri amachita malonda awo ngakhalenso maukwati ndi anthu a ku Mozambique.
Dedza ndi boma lina la dziko la Malawi. Dedza Golomoti escarpment ku Dedza. Bomali liri pa malire ndi maboma a Ntcheu, Lilongwe, Salima, Mangochi, Balaka Komanso Mozambique. Anthu ambiri amachita malonda awo ngakhalenso maukwati ndi anthu a ku Mozambique.